Numeri 19:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo atengereko wodetsedwayo mapulusa akupsererawo a nsembe yauchimo, nathirepo m'chotengera madzi oyenda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo atengereko wodetsedwayo mapulusa akupsererawo a nsembe yauchimo, nathirepo m'chotengera madzi oyenda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Woipitsidwayo amtengereko m'mbiya phulusa la nsembe yopsereza yopepesera machimo, ndipo aonjezemo madzi abwino atsikulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “Za munthu wodetsedwayo: ikani phulusa lochokera ku nsembe ya chiyeretso mu mtsuko ndi kuthiramo madzi abwino. Onani mutuwo |