Numeri 18:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo akuyesereninso nsembe yanu yokweza monga tirigu wa padwale, monga mopondera mphesa modzala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo akuyesereninso nsembe yanu yokweza monga tirigu wa padwale, monga mopondera mphesa modzala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Ndipo chopereka chanucho chidzaŵerengedwa ngati tirigu woyamba kucha amene anthu amapuntha, ndiponso mphesa zoyamba kucha zimene amapsinya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Chopereka chanucho chidzawerengedwa kwa inu ngati tirigu wochokera kopunthira kapena ngati mphesa zopsinya kuchokera kopsinyira mphesa. Onani mutuwo |