Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 18:14 - Buku Lopatulika

14 Zilizonse zoperekedwa chiperekere mu Israele ndi zako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Zilizonse zoperekedwa chiperekere m'Israele ndi zako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Chinthu chilichonse chimene anthu amapatulira Chauta m'dziko la Israele chikhale chanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 “Chilichonse mu Israeli chomwe chapatulidwira Yehova ndi chako.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 18:14
4 Mawu Ofanana  

Azidya nsembe yaufa, ndi nsembe yauchimo, ndi nsembe yopalamula; ndipo zilizonse zoperekedwa chiperekere mu Israele ndi zao.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,


koma potuluka m'chaka choliza lipenga, mundawo ukhale wopatulikira Yehova, ngati munda woperekedwa chiperekere kwa Mulungu; ukhale wakewake wa wansembe.


Koma asachigulitse kapena kuchiombola chinthu choperekedwa chiperekere kwa Mulungu, chimene munthu achipereka chiperekere kwa Yehova, chotengako ku zonse ali nazo, ngakhale munthu, kapena nyama, kapena munda wakewake; chilichonse choperekedwa chiperekere kwa Mulungu nchopatulika kwambiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa