Numeri 16:41 - Buku Lopatulika41 Koma m'mawa mwake khamu lonse la ana a Israele anadandaula pa Mose ndi Aroni, nati, Mwapha anthu a Yehova, inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Koma m'mawa mwake khamu lonse la ana a Israele anadandaula pa Mose ndi Aroni, nati, Mwapha anthu a Yehova, inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Koma m'maŵa mwake mpingo wonse wa Aisraele udaŵiringulira Mose ndi Aroni kuti, “Inu mwapha anthu a Chauta.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Tsiku lotsatira, gulu lonse la Aisraeli linatsutsana ndi Mose ndi Aaroni. Iwo anati, “Inu mwapha anthu a Yehova.” Onani mutuwo |