Numeri 16:37 - Buku Lopatulika37 Nena ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, kuti aphule mbale zofukiza pakati pa moto, nutaye makalawo uko kutali: pakuti zili zopatulika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Nena ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, kuti aphule mbale zofukiza pakati pa moto, nutaye makalawo uko kutali: pakuti zili zopatulika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 “Uza Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti achotse zofukizira lubani zija m'motomo, ndipo motowo aumwazire kutali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 “Uza Eliezara mwana wa Aaroni, wansembe kuti atenge zofukizirazo pakati pa mitembo yopsererayo ndipo amwazire makalawo kutali chifukwa zofukizirazo nʼzopatulika. Onani mutuwo |