Numeri 16:29 - Buku Lopatulika29 Akafa anthu awa monga amafa anthu onse, kapena akasungika monga amasungika anthu onse, Yehova sananditumize ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Akafa anthu awa monga amafa anthu onse, kapena akasungika monga amasungika anthu onse, Yehova sananditumize ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Anthu aŵa akafa monga m'mene amafera anthu onse, Mulungu osaŵalanga, ndiye kuti Chauta sadanditume ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ngati anthu awa afa ndi imfa ya chilengedwe ndi kuwachitikira zomwe zimachitikira munthu aliyense, ndiye kuti Yehova sananditume. Onani mutuwo |