Numeri 12:7 - Buku Lopatulika7 Satero mtumiki wanga Mose; ndiye wokhulupirika m'nyumba mwanga monse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Satero mtumiki wanga Mose; ndiye wokhulupirika m'nyumba mwanga monse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma sinditero ndi mtumiki wanga Mose, amene wakhala woyang'anira anthu anga onse a Israeli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma sinditero ndi Mose mtumiki wanga; Iyeyu ndi wokhulupirika mʼnyumba yanga yonse. Onani mutuwo |