Numeri 12:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Yehova anatsika mumtambo njo, naima pa khomo la chihema, naitana Aroni ndi Miriyamu; natuluka onse awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Yehova anatsika mumtambo njo, naima pa khomo la chihema, naitana Aroni ndi Miriyamu; natuluka onse awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chauta adatsika mu mtambo, naima pakhomo pa hema, ndipo adaitana Aroni ndi Miriyamu, tsono aŵiri onsewo adabweradi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tsono Yehova anatsika mu mtambo, nayima pa khomo la chihema. Kenaka anayitana Aaroni ndi Miriamu. Ndipo onse awiri atapita patsogolo, Onani mutuwo |