Numeri 10:36 - Buku Lopatulika36 Ndi pakupumula ili anati, Bwerani Yehova kwa zikwizikwi za Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndi pakupumula ili anati, Bwerani Yehova kwa zikwizikwi za Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Mtambowo ukaima, Mose ankati, “Inu Chauta, bwererani kwa Aisraele anu amene ali zikwi zosaŵerengeka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 “Pamene likupumula, ankanena kuti, “Bwererani, Inu Yehova, ku chinamtindi cha Aisraeli.” Onani mutuwo |