Numeri 10:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo kunachitika, chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, tsiku la makumi awiri la mweziwo, kuti mtambo unakwera kuchokera kwa chihema cha mboni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo kunachitika, chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, tsiku la makumi awiri la mweziwo, kuti mtambo unakwera kuchokera kwa Kachisi wa mboni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pa chaka chachiŵiri, mwezi wachiŵiri, tsiku la 20, mtambo udachoka pa chihema chaumboni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pa chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, tsiku la 20, mtambo unachoka pamwamba pa chihema cha umboni. Onani mutuwo |