Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:37 - Buku Lopatulika

37 owerengedwa ao a fuko la Benjamini, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu zisanu kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 owerengedwa ao a fuko la Benjamini, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu zisanu kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Benjamini, adapezeka kuti ali 35,400.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Benjamini chinali 35,400.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:37
7 Mawu Ofanana  

ndi a Benjamini: Eliyada ngwazi yamphamvu, ndi pamodzi ndi iye zikwi mazana awiri ogwira mauta ndi zikopa;


A ana a Benjamini, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


A ana a Dani, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu zisanu kudza mazana anai.


Iwo ndiwo ana a Benjamini monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi.


Ndipo anawerenga ana a Benjamini a m'mizinda tsiku lija amuna zikwi makumi awiri mphambu zisanu ndi chimodzi akusolola lupanga; osawerenga okhala mu Gibea, ndiwo amuna osankhika mazana asanu ndi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa