Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:31 - Buku Lopatulika

31 owerengedwa ao a fuko la Zebuloni, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 owerengedwa ao a fuko la Zebuloni, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Zebuloni, adapezeka kuti ali 57,400.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Zebuloni chinali 57,400.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:31
4 Mawu Ofanana  

A ana a Zebuloni, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


A ana a Yosefe, ndiwo a ana a Efuremu, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai.


Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa