Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:29 - Buku Lopatulika

29 owerengedwa ao a fuko la Isakara, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 owerengedwa ao a fuko la Isakara, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Isakara, adapezeka kuti ali 54,400.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Isakara chinali 54,400.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:29
4 Mawu Ofanana  

A ana a Isakara, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


A ana a Zebuloni, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai.


Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa