Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:27 - Buku Lopatulika

27 owerengedwa ao a fuko la Yuda, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zinai kudza mazana asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 owerengedwa ao a fuko la Yuda, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zinai kudza mazana asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Yuda, adapezeka kuti ali 74,600.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Yuda chinali 74, 600.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:27
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Yowabu anapereka kwa mfumu kuchuluka kwa anthu adawawerenga; ndipo mu Israele munali anthu zikwi mazana asanu ndi atatu, ngwazi zosolola lupanga; ndi anthu a Yuda ndiwo zikwi mazana asanu.


A ana a Yuda, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


A ana a Isakara, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Iwo ndiwo mabanja a Yuda monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa