Nehemiya 8:8 - Buku Lopatulika8 Nawerenga iwo m'buku m'chilamulo cha Mulungu momveka, natanthauzira, nawazindikiritsa chowerengedwacho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Nawerenga iwo m'buku m'chilamulo cha Mulungu momveka, natanthauzira, nawazindikiritsa chowerengedwacho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Aleviwo adaŵerenga buku la Malamulo a Mulungu momveka bwino, ndipo adatanthauzira mauwo kuti anthu amvetse bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iwo anawerenga buku la malamulo a Mulungu momveka bwino ndi kutanthauzira mawuwo kuti anthu amvetse bwino zowerengedwazo. Onani mutuwo |