Nehemiya 7:60 - Buku Lopatulika60 Antchito onse a m'kachisi, ndi ana a akapolo a Solomoni, ndiwo mazana atatu mphambu makumi asanu ndi anai kudza awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201460 Anetini onse, ndi ana a akapolo a Solomoni, ndiwo mazana atatu mphambu makumi asanu ndi anai kudza awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa60 Antchito onse a ku Nyumba ya Mulungu, kuphatikizapo zidzukulu za antchito a Solomoni, onse pamodzi analipo 392. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero60 Anthu onse ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi zidzukulu za antchito a Solomoni analipo 392. Onani mutuwo |