Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 7:43 - Buku Lopatulika

43 A Levi: ana a Yesuwa, a Kadimiyele, a ana a Hodeva, makumi asanu ndi awiri kudza anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 A Levi: ana a Yesuwa, a Kadimiyele, a ana a Hodeva, makumi asanu ndi awiri kudza anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 Alevi anali aŵa: a banja la Yesuwa ndi la Kadimiyele, ndiye kuti zidzukulu za Hodaviya, 74.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Alevi anali awa: A banja la Yesuwa ndi Kadimieli, ndiye kuti zidzukulu za Hodaviya 74.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:43
7 Mawu Ofanana  

Alevi: ana a Yesuwa, ndi Kadimiyele, ndiwo a ana a Hodaviya, makumi asanu ndi awiri mphambu anai.


ndi abale ao: Sebaniya, Hodiya, Kelita, Pelaya, Hanani,


Awa tsono ndi akulu a dziko okhala mu Yerusalemu; koma m'midzi ya Yuda yense anakhala pa cholowa chake m'midzi mwao, ndiwo Israele, ansembe, ndi Alevi, ndi antchito a m'kachisi, ndi ana a akapolo a Solomoni.


Ndi Alevi ndiwo Yesuwa, Binuyi, Kadimiyele, Serebiya, Yuda, ndi Mataniya; iye ndi abale ake amatsogolera mayamiko.


Ndi pambali pao anakonza Refaya mwana wa Huri, ndiye mkulu wa dera lina la dziko la Yerusalemu.


Ana a Harimu, chikwi chimodzi mphambu khumi limodzi kudza asanu ndi awiri.


Oimbira: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa