Nehemiya 7:34 - Buku Lopatulika34 Ana a Elamu winayo, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ana a Elamu winayo, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 A banja la Elamu wina 1,254. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ana a Elamu wina 1,254 Onani mutuwo |