Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 7:26 - Buku Lopatulika

26 Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Amuna a ku Betelehemu ndi a ku Netofa 188.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Anthu a ku Betelehemu ndi Netofa 188

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:26
7 Mawu Ofanana  

Zalimoni Mwahohi, Maharai Mnetofa;


Helebi mwana wa Baana Mnetofa, Itai mwana wa Ribai wa ku Gibea wa ana a Benjamini;


Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,


Ana a Gibiyoni, makumi asanu ndi anai kudza asanu.


Amuna a ku Anatoti, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.


pamenepo anadza kwa Gedaliya ku Mizipa, Ismaele mwana wa Netaniya, ndi Yohanani ndi Yonatani ana a Kareya, ndi Seraya mwana wa Tanumeti, ndi ana a Efayi wa ku Netofa, ndi Yezaniya mwana wa munthu wa ku Maaka, iwo ndi anthu ao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa