Nehemiya 7:24 - Buku Lopatulika24 Ana a Harifi, zana limodzi mphambu khumi ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ana a Harifi, zana limodzi mphambu khumi ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 A banja la Harifi 112. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Zidzukulu za Harifu 112 Onani mutuwo |