Nehemiya 7:21 - Buku Lopatulika21 Ana a Atere, a Hezekiya, makumi asanu ndi anai kudza asanu ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ana a Atere, a Hezekiya, makumi asanu ndi anai kudza asanu ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 A banja la Atere, ndiye kuti la Hezekiya, 98. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Zidzukulu za Ateri (kudzera mwa Hezekiya) 98 Onani mutuwo |