Nehemiya 7:12 - Buku Lopatulika12 Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 A banja la Elamu 1,254. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Zidzukulu za Elamu 1,254 Onani mutuwo |