Nehemiya 2:2 - Buku Lopatulika2 Ninena nane mfumu, Nkhope yako nja chisoni chifukwa ninji popeza sudwala? Ichi si chinthu china koma chisoni cha mtima. Pamenepo ndinachita mantha aakulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ninena nane mfumu, Nkhope yako nja chisoni chifukwa ninji popeza sudwala? Ichi si chinthu china koma chisoni cha mtima. Pamenepo ndinachita mantha akulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Apo mfumu idandifunsa kuti, “Kodi bwanji nkhope yako ili yakugwa, pamene sukudwala? Chimenechi si china, koma ndi chisoni chamumtima.” Pamenepo ndidaopa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tsono mfumu inandifunsa kuti, “Nʼchifukwa chiyani nkhope yako ikuoneka yachisoni pamene iwe sukudwala? Ichi si chinthu china koma chisoni cha mu mtima.” Ine ndinachita mantha kwambiri. Onani mutuwo |