Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 11:27 - Buku Lopatulika

27 ndi mu Hazara-Suwala, ndi mu Beereseba ndi midzi yake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 ndi m'Hazara-Suwala, ndi m'Beereseba ndi milaga yake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 ku Hazarisuwala, ku Beereseba ndi midzi yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Hazari-Suwali, Beeriseba ndi midzi yawo.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 11:27
9 Mawu Ofanana  

Ndipo Abrahamu analawira m'mamawa, natenga mkate ndi thumba la madzi, nampatsa Hagara, naika paphewa pake, ndi mwana, namchotsa iye: ndipo iye anamuka, nasocherera m'chipululu cha Beereseba.


Chifukwa chake anatcha malowo Beereseba: chifukwa pamenepo analumbira onse awiri.


Ndipo anatcha dzina lake Siba, chifukwa chake dzina la mzindawo ndi Beereseba kufikira lero lino.


Ndipo anakhala ku Beereseba, ndi Molada, ndi Hazara-Suwala,


ndi mu Yesuwa, ndi mu Molada, ndi Betepeleti,


ndi mu Zikilagi, ndi mu Mekona ndi midzi yake,


ndi Hazara-Suwala, ndi Beereseba, ndi Biziyotiya;


ndi Hazara-Suwala, ndi Bala, ndi Ezemu;


Pamenepo anatuluka ana onse a Israele, nuunjikana msonkhano kwa Yehova ku Mizipa ngati munthu mmodzi, kuyambira ku Dani mpaka Beereseba ndi dziko la Giliyadi lomwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa