Nehemiya 10:20 - Buku Lopatulika20 Magapiyasi, Mesulamu, Heziri, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Magapiyasi, Mesulamu, Heziri, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Magapiyasi, Mesulamu, Heziri, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Magipiyasi, Mesulamu, Heziri Onani mutuwo |
Ndipo Ezara mlembi anaima pa chiunda cha mitengo adachimangira msonkhanowo; ndi pambali pake padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseiya, kudzanja lamanja lake; ndi kudzanja lamanzere Pedaya, ndi Misaele, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.