Nehemiya 1:1 - Buku Lopatulika1 Mau a Nehemiya mwana wa Hakaliya. Kunali tsono mwezi wa Kisilevi, chaka cha makumi awiri, pokhala ine ku Susa kunyumba ya mfumu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mau a Nehemiya mwana wa Hakaliya. Kunali tsono mwezi wa Kisilevi, chaka cha makumi awiri, pokhala ine ku Susa kunyumba ya mfumu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Naŵa mau a Nehemiya, mwana wa Hakaliya: Pa mwezi wa Kisilevi, chaka cha 20 cha ufumu wa Arita-kisereksesi, pamene ndinali mu mzinda wa Susa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Awa ndi mawu a Nehemiya mwana wa Hakaliya: Pa mwezi wa Kisilevi, chaka cha makumi awiri, pamene ndinali mu mzinda wa Susa, Onani mutuwo |