Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 2:2 - Buku Lopatulika

2 Ndinati, Kuseka ndi masala; ndi chimwemwe kodi chichita chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndinati, Kuseka ndi masala; ndi chimwemwe kodi chichita chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Kukakhala kuseka, ndidati, “Imene ija ndi misala.” Chikakhala chisangalatso, ndidati, “Phindu lake nchiyani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Kuseka,” ndinati, “imeneyo ndi misala. Ndipo kodi chisangalalo chimabweretsa phindu lanji?”

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 2:2
6 Mawu Ofanana  

Ngakhale m'kuseka mtima uwawa; ndipo matsiriziro a chiphwete ndi chisoni.


Mtima wosekerera uchiritsa bwino; koma mzimu wosweka uphwetsa mafupa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa