Mika 1:6 - Buku Lopatulika6 Chifukwa chake ndidzaika Samariya ngati mulu wa miyala ya m'munda, ngati zooka m'munda wampesa; ndipo ndidzataya miyala yake m'chigwa, ndi kufukula maziko ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chifukwa chake ndidzaika Samariya ngati mulu wa miyala ya m'munda, ngati zooka m'munda wamphesa; ndipo ndidzataya miyala yake m'chigwa, ndi kufukula maziko ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono Chauta akuti, “Samariyayo ndidzamsandutsa bwinja, malo olimamo munda wamphesa. Miyala yake ndidzaitaya ku zigwa, ndipo maziko ake ndidzaŵafukula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Choncho Ine ndidzasandutsa Samariya kukhala bwinja, malo odzalamo mphesa. Miyala yake ndidzayitaya ku chigwa ndipo ndidzafukula maziko ake. Onani mutuwo |