Mika 1:4 - Buku Lopatulika4 Ndi mapiri adzasungunuka pansi pa Iye, ndi zigwa zidzang'ambika, ngati sera pamoto, ngati madzi otsanulidwa potsetsereka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndi mapiri adzasungunuka pansi pa Iye, ndi zigwa zidzang'ambika, ngati sera pamoto, ngati madzi otsanulidwa potsetseremba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mapiriwo akusungunuka ngati phula pa moto. Akuyenderera m'zigwa ngati madzi ochokera m'phiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mapiri akusungunuka pansi pake, ndipo zigwa zikugawikana ngati phula pa moto, ngati madzi ochokera mʼphiri. Onani mutuwo |