Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 9:21 - Buku Lopatulika

21 pakuti analikunena mwa iye yekha, Ngati ndingakhudze chofunda chake chokha ndidzachira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 pakuti analikunena mwa iye yekha, Ngati ndingakhudze chofunda chake chokha ndidzachira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Mumtima mwake ankaganiza kuti, “Ndikangokhudza ngakhale chovala chake chokhacho, ndichira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Iyeyo anati mwa iye yekha, “Nditangokhudza kasonga ka mkanjo wake, ine ndidzachiritsidwa.”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 9:21
6 Mawu Ofanana  

ndipo anampempha Iye, kuti akhudze mphonje yokha ya chovala chake; ndipo onse amene anamkhudza anachiritsidwa.


pakuti adawachiritsa ambiri; kotero kuti onse akukhala nazo zowawa anakanikiza Iye, kuti akamkhudze.


ndi khamu lonse lija linafuna kumkhudza Iye; chifukwa munatuluka mphamvu mwa Iye, nkuchiritsa onsewa.


kotero kuti anamuka nazo kwa odwala nsalu zopukutira ndi za pantchito, zochokera pathupi pake, ndipo nthenda zinawachokera, ndi ziwanda zinatuluka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa