Mateyu 8:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo iwo anadza, namuutsa Iye, nanena, Ambuye, tipulumutseni, tilikutayika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo iwo anadza, namuutsa Iye, nanena, Ambuye, tipulumutseni, tilikutayika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pamenepo ophunzira ake aja adamudzutsa, adati, “Ambuye, tipulumutseni, tikumiratu!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ophunzira ake anapita namudzutsa nati, “Ambuye! Tipulumutseni! Tikumira!” Onani mutuwo |