Mateyu 8:12 - Buku Lopatulika12 koma anawo a Ufumu adzatayidwa kumdima wakunja; komweko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 koma anawo a Ufumu adzatayidwa kumdima wakunja; komweko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma chonsecho amene akadayenera kukhala mu Ufumuwo, adzaŵaponya kunja, ku mdima. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano chifukwa cha zoŵaŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma eni ake ufumuwo adzaponyedwa ku mdima wakunja kumene kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.” Onani mutuwo |