Mateyu 7:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo upenya bwanji kachitsotso kali m'diso la mbale wako, koma mtanda uli m'diso la iwe mwini suuganizira? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo upenya bwanji kachitsotso kali m'diso la mbale wako, koma mtanda uli m'diso la iwe mwini suuganizira? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Umaoneranji kachitsotso kamene kali m'maso mwa mnzako, koma osaganizako za chimtengo chimene chili m'maso mwako momwe? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 “Chifukwa chiyani iwe uyangʼana kachitsotso ka mʼdiso la mʼbale wako koma susamalira chimtengo chili mʼdiso mwako? Onani mutuwo |