Mateyu 5:36 - Buku Lopatulika36 Kapena usalumbire kumutu wako, chifukwa sungathe kuliyeretsa mbuu kapena kulidetsa bii tsitsi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Kapena usalumbire kumutu wako, chifukwa sungathe kuliyeretsa mbu kapena kulidetsa bii tsitsi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Usalumbire ngakhale pa mutu wako, pakuti sungathe kusandulitsa ndi tsitsi limodzi lomwe kuti likhale loyera kapena lakuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Ndipo musalumbire ndi mutu wanu chifukwa simungathe kuyeretsa ngakhale kudetsa tsitsi limodzi. Onani mutuwo |