Mateyu 27:43 - Buku Lopatulika43 Amakhulupirira Mulungu; Iye ampulumutse tsopano, ngati amfuna; pakuti anati, Ine ndine Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Amakhulupirira Mulungu; Iye ampulumutse tsopano, ngati amfuna; pakuti anati, Ine ndine Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Ankadalira Mulungu; ampulumutsetu tsopano Mulunguyo, ngati amamkondadi; paja ankati, Ndine Mwana wa Mulungu!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Amadalira Mulungu, mulekeni Mulunguyo amupulumutse tsopano ngati akumufuna pakuti anati, ‘Ndine Mwana wa Mulungu.’ ” Onani mutuwo |