Mateyu 26:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo kuyambira pamenepo iye anafunafuna nthawi yabwino yakuti ampereke Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo kuyambira pamenepo iye anafunafuna nthawi yabwino yakuti ampereke Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono kuyambira pomwepo iye adayamba kufunafuna mpata womuperekera kwa iwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kuyambira pamenepo Yudasi anafunafuna nthawi yabwino yoti amupereke Yesu. Onani mutuwo |