Mateyu 24:51 - Buku Lopatulika51 nadzamdula, nadzaika pokhala pake ndi anthu onyenga; pomwepo padzakhala kulira ndi kukukuta mano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 nadzamdula, nadzaika pokhala pake ndi anthu onyenga; pomwepo padzakhala kulira ndi kukukuta mano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Choncho adzamlanga koopsa, ndipo adzamtaya ku malo a anthu achiphamaso. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Adzamulanga koopsa ndipo adzamuyika kokhala anthu achiphamaso, kumene kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.” Onani mutuwo |