Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 24:23 - Buku Lopatulika

23 Pomwepo munthu akanena kwa inu, Onani, Khristu ali kuno, kapena uko musamvomereze;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Pomwepo munthu akanena kwa inu, Onani, Khristu ali kuno, kapena uko musamvomereze;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 “Pa nthaŵi imeneyo wina akadzakuuzani kuti, ‘Ali panotu Khristu uja! Uyo ali apoyo!’ musadzakhulupirire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Pa nthawi imeneyo ngati wina adzati kwa inu, ‘Onani, Khristu ali pano!’ Kapena, ‘Uyo ali ukoyo!’ Musakhulupirire.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 24:23
6 Mawu Ofanana  

Ndipo pamenepo wina akati kwa inu, Onani Khristu ali pano; kapena, Onani, uko; musavomereze;


Ndipo Iye anati, Yang'anirani musasocheretsedwe; pakuti ambiri adzadza m'dzina langa, nadzanena, Ndine amene; ndipo, Nthawi yayandikira; musawatsate pambuyo pao.


Ndadza Ine m'dzina la Atate wanga, ndipo simundilandira Ine; akadza wina m'dzina lake la iye mwini, iyeyu mudzamlandira.


Koma kenturiyo anakhulupirira watsigiro ndi mwini ngalawa makamaka, wosasamala mau a Paulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa