Mateyu 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Herode mfumuyo pakumva ichi anavutika, ndi Yerusalemu yense pamodzi naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Herode mfumuyo pakumva ichi anavutika, ndi Yerusalemu yense pamodzi naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mfumu Herode atamva zimenezi, adavutika kwambiri ndipo anthu ena onse a m'Yerusalemu nawonso adavutika nazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mfumu Herode atamva zimenezi, anavutika mu mtima kwambiri pamodzi ndi anthu onse a mu Yerusalemu. Onani mutuwo |