Mateyu 18:23 - Buku Lopatulika23 Chifukwa chake Ufumu wa Kumwamba ufanizidwa ndi munthu, mfumu, amene anafuna kuwerengera nao akapolo ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Chifukwa chake Ufumu wa Kumwamba ufanizidwa ndi munthu, mfumu, amene anafuna kuwerengera nao akapolo ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Tsono Ufumu wakumwamba tingaufanizire motere: Panali mfumu ina imene idaaitanitsa antchito ake kuti iwonenso bwino ngongole zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 “Nʼchifukwa chake, ufumu wakumwamba ukufanana ndi mfumu imene inafuna kuti antchito ake abweze ngongole. Onani mutuwo |