Mateyu 17:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo onani, Mose ndi Eliya anaonekera kwa iwo, alinkulankhula ndi Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo onani, Mose ndi Eliya anaonekera kwa iwo, alinkulankhula ndi Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nthaŵi yomweyo ophunzira aja adaona Mose ndi Eliya akulankhula naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nthawi yomweyo Mose ndi Eliya anaonekera kwa iwo akuyankhulana ndi Yesu. Onani mutuwo |