Mateyu 17:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Yesu anamdzudzula; ndipo chiwanda chinatuluka mwa iye; ndipo mnyamatayo anachira kuyambira nthawi yomweyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Yesu anamdzudzula; ndipo chiwanda chinatuluka mwa iye; ndipo mnyamatayo anachira kuyambira nthawi yomweyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Atatero, Yesu adazazira mzimu woipawo, ndipo udatuluka mwa mnyamatayo. Pompo iye adachira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yesu anadzudzula chiwandacho ndipo chinatuluka mwa mnyamatayo ndipo anachira nthawi yomweyo. Onani mutuwo |