Mateyu 13:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo tsono mverani inu fanizolo la wofesa mbeu uja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo tsono mverani inu fanizolo la wofesa mbeu uja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 “Tsono inu mumvetse bwino tanthauzo lake la fanizo la munthu wofesa mbeu lija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 “Tamverani tsono zimene fanizo la wofesa litanthauza: Onani mutuwo |