Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 13:13 - Buku Lopatulika

13 Chifukwa chake ndiphiphiritsira iwo m'mafanizo; chifukwa kuti akuona samaona, ndi akumva samamva, kapena samadziwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Chifukwa chake ndiphiphiritsira iwo m'mafanizo; chifukwa kuti akuona samaona, ndi akumva samamva, kapena samadziwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Tsono anthuŵa ndimalankhula nawo m'mafanizo, chifukwa ngakhale amapenya, komabe saona, ndipo ngakhale amamva, komabe samva kwenikweni kapena kumvetsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ichi ndi chifukwa chake ndimayankhula kwa iwo mʼmafanizo: “Ngakhale akupenya koma saona, ngakhale akumva koma samvetsetsa kapena kuzindikira.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 13:13
12 Mawu Ofanana  

Iwo sadziwa, kapena kuzindikira, chifukwa pamaso mwao papakidwa thope, kuti sangaone, ndi m'mitima mwako kuti sangadziwitse.


Tamvanitu ichi, inu anthu opusa, ndi opanda nzeru; ali ndi maso koma osaona, ali ndi makutu koma osamva;


Wobadwa ndi munthu iwe, ukhala pakati pa nyumba yampanduko, yokhala nao maso akuonera, koma osaona; ndi makutu akumvera, koma osamva; pakuti iwo ndiwo nyumba yampanduko.


Pamenepo ndinati, Ha, Ambuye Yehova! Anandinena, Wonena mafanizo uyu.


Koma maso anu ali odala, chifukwa apenya; ndi makutu anu chifukwa amva.


monga kunalembedwa kuti, Mulungu anawapatsa mzimu watulo, maso kuti asapenye, ndi makutu kuti asamve, kufikira lero lino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa