Mateyu 12:26 - Buku Lopatulika26 ndipo ngati Satana amatulutsa Satana, iye agawanika pa yekha; ndipo udzakhala bwanji ufumu wake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndipo ngati Satana amatulutsa Satana, iye agawanika pa yekha; ndipo udzakhala bwanji ufumu wake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Ngati a mu ufumu wa Satana atulutsana okhaokha, ndiye kuti agaŵikana. Nanga Satanayo ufumu wake ungalimbe bwanji? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ngati Satana atulutsa Satana, iye adzigawa yekha. Nanga ufumu wake ungayime bwanji? Onani mutuwo |