Mateyu 11:20 - Buku Lopatulika20 Pomwepo Iye anayamba kutonza mizindayo, m'mene zinachitidwa zambiri za ntchito zamphamvu zake, chifukwa kuti siinatembenuke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pomwepo Iye anayamba kutonza midziyo, m'mene zinachitidwa zambiri za ntchito zamphamvu zake, chifukwa kuti siinatembenuke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pambuyo pake Yesu adayamba kudzudzula midzi imene Iye adaaichitira zamphamvu zochuluka. Adaidzudzula chifukwa anthu ake anali osatembenuka mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Pamenepo Yesu anayamba kudzudzula mizinda imene zodabwitsa zake zambiri zinachitikamo, chifukwa chakuti sinatembenuke mtima. Onani mutuwo |