Mateyu 10:29 - Buku Lopatulika29 Kodi mpheta ziwiri sizigulidwa kakobiri? Ndipo imodzi ya izo siigwa pansi popanda Atate wanu: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Kodi mpheta ziwiri sizigulidwa kakobiri? Ndipo imodzi ya izo siigwa pansi popanda Atate wanu: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Suja amagulitsa atimba aŵiri kandalama kamodzi? Komabe palibe ndi m'modzi yemwe amene angagwe pansi, Atate anu osadziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Kodi suja amagulitsa mbalame ziwiri ndi ndalama imodzi? Koma palibe imodzi ya izo imene idzagwa pansi wopanda chifuniro cha Atate anu. Onani mutuwo |