Mateyu 10:27 - Buku Lopatulika27 Chimene ndikuuzani inu mumdima, tachinenani poyera; ndi chimene muchimva m'khutu, muchilalikire pa matsindwi a nyumba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Chimene ndikuuzani inu mumdima, tachinenani poyera; ndi chimene muchimva m'khutu, muchilalikire pa machindwi a nyumba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Zimene ndikukuuzirani m'chibisibisi, inu mukazilankhulire poyera, ndipo zimene mukuzimvera m'manong'onong'o, inu mukazilalikire pa madenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Chimene ndikuwuzani Ine mu mdima, muchiyankhule poyera; chimene akunongʼonezani mʼkhutu, muchilalikire muli pa denga. Onani mutuwo |