Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:18 - Buku Lopatulika

18 Ndipo anayesa Mulungu mumtima mwao ndi kupempha chakudya monga mwa kulakalaka kwao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo anayesa Mulungu mumtima mwao ndi kupempha chakudya monga mwa kulakalaka kwao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Iwo adayesa Mulungu m'mitima mwao, pomuumiriza kuti aŵapatse chakudya chimene ankakhumba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ananyoza Mulungu mwadala pomuwumiriza kuti awapatse chakudya chimene anachilakalaka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:18
10 Mawu Ofanana  

Pamene makolo anu anandisuntha, anandiyesa, anapenyanso chochita Ine.


Pamenepo anthu anatsutsana ndi Mose, nati, Tipatseni madzi timwe. Koma Mose ananena nao, Mutsutsana nane bwanji? Muyeseranji Yehova?


Ndipo anatcha dzina la malowo Masa, ndi Meriba, chifukwa cha kutsutsana kwa ana a Israele; popezanso anayesa Yehova, ndi kuti, Kodi Yehova ali pakati pa ife, kapena iai?


Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa nacho chilakolako; ndi ana a Israele omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?


Koma zinthu izi zinachitika, zikhale zotichenjeza ife, kuti tisalakalake zoipa ife, monganso iwowo analakalaka.


Kapena tisayese Ambuye, monga ena a iwo anayesa, naonongeka ndi njoka zija.


Musamayesa Yehova Mulungu wanu, monga munamyesa mu Masa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa