Masalimo 71:17 - Buku Lopatulika17 Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga; ndipo kufikira lero ndilalikira zodabwitsa zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga; ndipo kufikira lero ndilalikira zodabwitsa zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga, ndipo ndikulalikabe ntchito zanu zodabwitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Kuyambira ubwana wanga, Inu Mulungu mwakhala mukundiphunzitsa, ndipo mpaka lero ine ndikulengeza za ntchito zanu zodabwitsa Onani mutuwo |